Yesu waatana alovi anayi
18 Yesu yapo wamaenda mphepete mwa nyanja ya Galilaya wadaona abale awili, Simoni uyo wamatanidwa Petulo ni Anduleya. Amavuwa njhomba mnyanja kwa makoka yawo. 19 Yesu wadaakambila, "Majhani nichateni! Nane sinikuchiteni mukhale opeleka wandhu kwa Mnungu."