34 Maliya wadamuyangha ni kumfunjha mtumiki wa kumwamba wa Mnungu, "Sivikhozekane bwanji vindhu ivi, pakuti sinidapezane chithupi ni wammuna?" 35 Mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadamuyangha Maliya, "Mzimu woyela siukujhele iwe, ni mphavu zake uyo wali kumwamba kupunda sizikuvinikile iwe ngati chitunjhi. Chimwecho, ni Woyela uyo siwabadwe siwatanidwe Mwana wa Mnungu. 36 Ata mbale wako Elizabeti uyo wamatanidwa wambende, chipano wali ni pathupi pa miyezi sita, ingakhale iye ni mzee kupunda. 37 Mate yake palibe chindhu icho sichikhozeka kwa Mnungu." 38 Maliya wadayangha, "Ine ni mbowa wa Ambuye, mawu yaya yachitike ngati umo mwakambila." Ndiipo mtumiki wa kumwamba wadachokapo.