Pular para o conteúdo
Publicidade

MASALIMO 139

11 Ndikanena kuti, "Zoonadi, mdima udzandibisa ndithu

ndipo kuwunika kukhale mdima mondizungulira,"

12 komabe mdimawo sudzakhala mdima kwa Inu;

usiku udzawala ngati masana,

pakuti mdima uli ngati kuwunika kwa Inu.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também