Pular para o conteúdo
Publicidade

MASALIMO 65

1 Matamando akudikira Inu Mulungu mu Ziyoni;

kwa inu malumbiro athu adzakwaniritsidwa.

2 Inu amene mumamva pemphero,

kwa inu anthu onse adzafika.

3 Pamene tinathedwa nzeru ndi machimo,

Inu munakhululukira mphulupulu zathu.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também