14 Iwo adzaberekabe zipatso mu ukalamba wawo,
adzakhala anthete ndi obiriwira,
15 kulengeza kuti, "Yehova ndi wolungama;
Iye ndiye Thanthwe langa, ndipo mwa Iye mulibe choyipa."